BELIEVE IN THE LOVE AND SPIRIT OF THE CATHOLIC CHURCH
AN INCLUSIVE COMMUNITY FOR ALL WHO
WELCOMING YOU HOME
Our Devotions and Intercessions are made through the blessed Virgin Mary, Our Lady of Africa, the Patron Saint of the Cathedral. we Invoke the Blessed Virgin Mary, who watches over Africa and intercede for all her children throughout the world.
.jpeg)


NEXT EVENTS
June
Thursday, 4th June 2026
There will be a Eucharistic talk and Adoration in the afternoon, in preparation for Corpus Christ. Let us plan to attend this important session.
-
(Padzakhala maphunziro a Ukalisitiya komanso kupembedza Ambuye Yesu okhala mu Ukaristia Lachinayi, pa 4 Juni 2026, masana, pokonzekera mwambo wa chikuku.)
SUNDAY, JUNE 7TH 2026
Tsiku la Chikuku
Patsikuli Misa zidzakhala monga mwanthawi zonse kupatula Misa ya Chilatini yomwe siidzakhalapo. Misa ya Chilatini idzakhalapo pa 14th June, 2026. Welengani zambiri apa.
Misa yathu ya Chichewa idzakhalira ku Podium nthawi ya 10 koloko yomwe idzatsogozane ndi Mwambo woyenda ndi Chikuku.
Solemnity of the Body and Blood
of Our Lord Jesus Christ
The 10:00 a.m. Mass will be celebrated at the Podium, followed by a procession. There will be no Latin Mass on that day; instead, it will be held on 14th June 2026.
Announcent
The Parish would like to congratulate our boys and girls who wrote the MCCB Mock Examination and have passed.
The list of successful candidates has been posted here. The entrance examinations for secondary schools will take place on 20th June 2026 at St. Padre Pio Secondary School in Area 49. For more details, please consult the parish office.
Liturgy
MPHAKATI WA ST. PETER ndi omwe ukuyendetsa Chipembedzo sabata lino. Mulungu otsatira MPHAKATI WA ST. TELEZA ndi omwe udzatsogolere Chipembedzo sabata la mawa.
In the Spirit of active participation in liturgy, the leaders of next week in liturgy - The Holy Trinity Sunday - will be the East African community.
CHOIR YA YOUTH ndi yomwe idzatsogolere nyimbo pa Lamulungu la Utatu Woyera.












