
Bambo Makina Alimbikitsa Andende Kukhala Ndi Chikhulupiliro
Akayidi andende ya Maula ku Lilongwe alimbikitsidwa kuti akhale odalira Mulungu pa moyo wawo watsiku ndi tsiku. Bambo mthandizi a parishiyi, bambo Peter Makina ndi omwe alimbikitsa andendewa pamwambo wansembe ya




